Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 March tsamba 5
  • Mfumu Solomo Inasankha Zinthu Mopanda Nzeru

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mfumu Solomo Inasankha Zinthu Mopanda Nzeru
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Solomo Anali Mfumu Yanzeru
    Kodi Baibulo Lili Ndi Uthenga Wotani?
  • Kodi Solomo Ndi Chitsanzo Chabwino Kapena Choipa?
    Nsanja ya Olonda—2011
  • Muzilimbikitsa Abale ndi Alongo Anu Akakumana ndi Mavuto
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • “Khulupirirani Yehova Mulungu Wanu”
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 March tsamba 5
Mfumu Solomo ikuganizira mozama. Zithunzi: 1. Mzinda wokhala ndi mpanda wolimba. 2. Mahatchi ndi magaleta. 3. Amuna awiri akugwira mwakhama ntchito yomanga khoma la miyala.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mfumu Solomo Inasankha Zinthu Mopanda Nzeru

[Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 2 Mbiri.]

Solomo anasonkhanitsa mahatchi ndi magaleta ochokera ku Iguputo (De 17:15, 16; 2Mb 1:14, 17)

Pankafunika anthu komanso mizinda yambiri kuti asamalire mahatchi komanso magaletawa (2Mb 1:14; it-1 174 ¶5; 427)

Ngakhale kuti anthu anakhala moyo wosangalala mu zaka zoyambirira za ulamuliro wa Solomo, iwo anagalukira mu ufumu wa Rehobowamu chifukwa iye anawonjezera goli lolemera lomwe anali nalo. (2Mb 10:3, 4, 14, 16) Nthawi zonse zomwe timasankha zimakhala ndi zotsatirapo zake.​—Aga 6:7.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena