Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsamba 4
  • “Khulupirirani Yehova Mulungu Wanu”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Khulupirirani Yehova Mulungu Wanu”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Muziona Ena Mmene Yehova Amawaonera
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Kodi Ndi pa Nthawi Iti Pamene Tiyenera Kudalira Yehova?
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • ‘Mtima Wanga Udzakhala Pamenepa Nthawi Zonse’
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • B8 Kachisi Amene Solomo Anamanga
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 May tsamba 4

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Khulupirirani Yehova Mulungu Wanu”

Yehosafati limodzi ndi anthu a ku Yuda ataopsezedwa, anapempha Yehova kuti awathandize (2Mb 20:12, 13; w14 12/15 23 ¶8)

Yehova analimbikitsa anthu ake ndipo anawapatsa malangizo omveka bwino (2Mb 20:17)

Yehova anapulumutsa anthu ake chifukwa anamukhulupirira (2Mb 20:21, 22, 27; w21.11 16 ¶7)

Kagulu ka abale ndi alongo asonkhana m’nyumba ndipo apolisi ovala zodzitetezera komanso okhala ndi mfuti athyola nyumbayo n’kulowa.

Gogi akadzaukira anthu a Mulungu pa chisautso chachikulu, anthu amene amakhulupirira Yehova komanso kudalira anthu amene iye anawasankha kuti azititsogolera, sadzachita mantha.​—2Mb 20:20

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena