Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 March tsamba 6
  • ‘Mtima Wanga Udzakhala Pamenepa Nthawi Zonse’

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • ‘Mtima Wanga Udzakhala Pamenepa Nthawi Zonse’
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • “Khulupirirani Yehova Mulungu Wanu”
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • B8 Kachisi Amene Solomo Anamanga
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Muzitsatira Malangizo Anzeru
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Anagwira Ntchito Mwamphamvu Komanso ndi Mtima Wonse
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 March tsamba 6

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

‘Mtima Wanga Udzakhala Pamenepa Nthawi Zonse’

Yehova anasankha kachisi wake (2Mb 7:11, 12)

Yehova ananena kuti mtima wake udzakhalabe kumeneko nthawi zonse, zomwe zikusonyeza kuti adzapitiriza kuchita chidwi ndi zinthu zimene zikuchitika panyumba yodziwika ndi dzina lake (2Mb 7:16; w02 11/15 5 ¶1)

Ngati atasiya kutumikira Yehova “ndi mtima wawo wonse,” iye adzalola kuti kachisi awonongedwe (2Mb 6:14; 7:19-21; it-2 1077-1078)

Zithunzi zosonyeza: njira zogwiritsa ntchito polambira. 1. M’bale akupemphera. 2. Mlongo akupereka ndemanga pamisonkhano. 3. Banja likulalikira limodzi. 4. M’bale akugwira ntchito yoyeretsa panyumba ya Ufumu. 5. M’bale akuchita kulambira kwa pabanja limodzi ndi mkazi komanso ana ake awiri. 6. Mlongo akuwerenga Baibulo. 7. Mlongo akuponya ndalama mu bokosi la zopereka.

Pamene ankapereka kachisi, anthu ankaganiza kuti mtima wawo udzakhala pa kachisipo nthawi zonse. Koma chomvetsa chisoni n’chakuti pang’ono ndi pang’ono anthuwa anasiya kutumikira Yehova ndi mtima wawo wonse.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndikusonyeza bwanji kuti ndimatumikira Yehova ndi mtima wonse?’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena