Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 July tsamba 11
  • Anagwira Ntchito Mwamphamvu Komanso ndi Mtima Wonse

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Anagwira Ntchito Mwamphamvu Komanso ndi Mtima Wonse
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Nzeru Ndi Zamtengo Wapatali
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Solomo Amanga Kachisi
    Bukhu Langa la Nkhani za Baibulo
  • Solomo Anapemphera Modzichepetsa Komanso Mochokera Pansi pa Mtima
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nyumba ya Yehova
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 July tsamba 11
Pa nthawi yomanga kachisi, Mfumu Solomo akumvetsera mwatcheru kwa mmisiri amene akumufotokozera pulani ya nyumba imene akumangayo.

Mfumu Solomo ikuona mmene ntchito yomanga kachisi ikuyendera

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Anagwira Ntchito Mwamphamvu Komanso ndi Mtima Wonse

Solomo anagwiritsa ntchito zinthu zabwino kwambiri pomanga kachisi (1Mf 5:6, 17; w11 2/1 15)

Aisiraeli ambiri anagwira nawo ntchitoyi (1Mf 5:13-16; it-1 424; it-2 1077 ¶1)

Solomo ndi Aisiraeli anagwira mwakhama ntchitoyi kwa zaka 7 (1Mf 6:38; onani chithunzi chapachikuto)

Solomo ndi Aisiraeli anakwanitsa kumanga kachisi wokongola woti azilambiriramo Yehova chifukwa chakuti ankamukonda kwambiri. Koma n’zomvetsa chisoni kuti mibadwo imene inabwera pambuyo pawo, inasiya kulambira Yehova ndi mtima wonse. Iwo anasiya kusamalira kachisi ndipo kenako kachisiyo anawonongedwa.

Abale ndi alongo akukonza m’Nyumba ya Ufumu mosangalala. Kumbuyo kwawo, ena akucheza, ena akuponya ndalama m’bokosi la zopereka ndipo ena akuika mabuku pashelefu.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndikuchita zotani kuti ndipitirizebe kulambira Yehova ndi mtima wonse?’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena