Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 July tsamba 10
  • Nzeru Ndi Zamtengo Wapatali

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Nzeru Ndi Zamtengo Wapatali
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Mumagwiritsa Ntchito “Nzeru Yochokera Kumwamba” pa Moyo Wanu?
    Yandikirani Yehova
  • Solomo Anapemphera Modzichepetsa Komanso Mochokera Pansi pa Mtima
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Anagwira Ntchito Mwamphamvu Komanso ndi Mtima Wonse
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Solomo Anali Mfumu Yanzeru
    Kodi Baibulo Lili Ndi Uthenga Wotani?
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 July tsamba 10
Mfumu Solomo ikuweruza mlandu wa mahule awiri amene onse akunena kuti mwana ndi wawo.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Nzeru Ndi Zamtengo Wapatali

Solomo anapempha nzeru kwa Yehova (1Mf 3:7-9; w11 12/15 8 ¶4-6)

Yehova anasangalala ndi zimene Solomo anapempha (1Mf 3:10-13)

Aisiraeli ankakhala mwabata chifukwa chakuti Solomo ankagwiritsa ntchito nzeru zimene Mulungu anamupatsa (1Mf 4:25)

Kukhala wanzeru kumatanthauza kudziwa zinthu ndi kuzimvetsa bwinobwino kenako n’kuzigwiritsa ntchito moyenera. Nzeru ndi zamtengo wapatali kuposa golide. (Miy 16:16) Kuti tipeze nzeru tiyenera kumupempha Mulungu, kumamuopa, kukhala odzichepetsa komanso kuphunzira mozama Mawu ake.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena