Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 March tsamba 12
  • Muzitsatira Malangizo Anzeru

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muzitsatira Malangizo Anzeru
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Akanatha Kusangalatsa Mulungu
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2018
  • N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kupempha Malangizo?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2025
  • ‘Mtima Wanga Udzakhala Pamenepa Nthawi Zonse’
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Mfumu Solomo Inasankha Zinthu Mopanda Nzeru
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 March tsamba 12

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muzitsatira Malangizo Anzeru

Rehobowamu anafunika kusankha zochita (2Mb 10:1-4; w18.06 13 ¶3)

Rehobowamu anafunsira malangizo (2Mb 10:6-11; w01 9/1 28-29)

Rehobowamu ndi anthu ena anakumana ndi mavuto chifukwa iye sanatsatire malangizo anzeru (2Mb 10:12-16; it-2 768 ¶1)

Mlongo wachitsikana akumvetsera mwachidwi pamene mlongo wachikulire akulankhula ku malo odyera.

Chifukwa cha luso komanso msinkhu wawo, Akhristu olimba mwauzimu nthawi zina akhoza kudziwiratu mmene zinthu zingathere.​—Yob 12:12.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndi ndani mumpingo amene angandipatse malangizo abwino?’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena