Yobu akusonyeza anthu ovutika chikondi chokhulupirika
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Kodi Muli ndi Mbiri Ngati ya Yobu?
Yobu ankapatsidwa ulemu ndi anthu ena (Yob 29:7-11)
Yobu ankadziwika kuti ankasonyeza anthu ovutika chikondi chokhulupirika (Yob 29:12, 13; w02 5/15 22 ¶19; onani chithunzi chapachikuto)
Yobu ankachita zinthu mwachilungamo (Yob 29:14; it-1 655 ¶10)
Kukhala ndi mbiri yabwino n’kofunika kwambiri. (w09 2/1 15 ¶3-4) Timakhala ndi mbiri yabwino ngati kwanthawi yaitali tasonyeza kuti timachita zinthu zoyenera
DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndi makhalidwe ati amene ndimadziwika nawo?’