Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • wp21 No. 2 tsamba 3
  • Tikufunikira Dziko Labwino

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Tikufunikira Dziko Labwino
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Baibulo Limati Chiyani pa Nkhani ya Miliri?
    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
  • Kodi Inuyo Mungakonde Kusintha Zinthu Ziti?
    Galamukani!—2012
  • Kodi Chikuchitika N’chiyani ndi Nyengoyi?
    Galamukani!—2003
  • Kodi Anthu Adzasiya Liti Kumenya Nkhondo?—Zimene Baibulo Limanena
    Nkhani Zina
Onani Zambiri
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2021
wp21 No. 2 tsamba 3
Munthu waonera nkhani zomvetsa chisoni ndipo akuyang’ana kumbali. Wasokonezeka chifukwa choona zinthu zokhumudwitsa monga nkhondo, matenda umphawi komanso zachiwawa.

Tikufunikira Dziko Labwino

A António Guterres omwe ndi mlembi wamkulu wa bungwe la United Nations ananena kuti: “Tikukhala m’dziko lodzaza ndi mavuto.” Kodi inunso mukuona choncho?

Nkhani zimene timamvetsera, kuonera ndi kuwerenga, zimakhala ndi zinthu zambiri zodetsa nkhawa monga:

  • Matenda ndi miliri

  • Ngozi za m’chilengedwe

  • Umphawi ndi njala

  • Kuonongeka kwa mpweya ndi madzi komanso kutentha kwa dziko

  • Kuphwanya malamulo, zachiwawa ndiponso zachinyengo

  • Nkhondo

Mpake kuti tikufunikira dziko labwino. Dziko limene mudzakhale

  • Anthu athanzi labwino

  • Chitetezo

  • Chakudya chokwanira

  • Mpweya ndi madzi abwino

  • Chilungamo chenicheni

  • Mtendere wochuluka

Kodi tikamanena kuti dziko labwino tikutanthauza chiyani?

Kodi n’chiyani chimene chidzachitikire dziko limene tikukhalamoli?

Kodi tingatani kuti tidzakhale m’dziko labwino?

Magaziniyi ifotokoza mayankho otonthoza ochokera m’Baibulo a mafunso amenewa ndi enanso.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena