Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w23 June tsamba 32
  • Nkhani Zina Zopezeka mu ”Nsanja ya Olonda” Yophunzira

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Nkhani Zina Zopezeka mu ”Nsanja ya Olonda” Yophunzira
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Zimene Mungapezenso Pawebusaiti
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2023
  • Magazini Yophunzira Yatsopano ya Nsanja ya Olonda
    Nsanja ya Olonda—2008
  • Mungaphunzirenso Izi
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2023
  • Nkhani Zothandiza mu Utumiki
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2013
Onani Zambiri
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2023
w23 June tsamba 32

Nkhani Zina Zopezeka mu Nsanja ya Olonda Yophunzira

Ofalitsa ambiri amagwiritsa ntchito JW Library pokonzekera misonkhano ndipo amaona kuti imawathandiza kupeza mosavuta nkhani iliyonse yophunzira. Koma magazini yophunzira nthawi zambiri imakhalanso ndi nkhani zina zomwe ndi chakudya chauzimu. Kodi mungapeze bwanji nkhanizi pa JW Library kuti zizikuthandizani?

  • Kumapeto kwa nkhani zonse zophunzira kumakhala kamutu kakuti “Zinanso Zimene Mungawerenge.” Pansi pa kamutu kameneka, dinani pamene alemba kuti “Nkhani zina m’magaziniyi.” Mukapita pa mbali ya “Zimene Zili M’magaziniyi,” muona mitu komanso manambala a nkhani zophunzira. Kenako mungasankhe nkhani zina zomwe si zophunzira kuti muwerenge.

  • Pa tsamba loyamba la JW Library, pa gawo lakuti “What’s New,” pangani dawunilodi magazini iliyonse yatsopano ya Nsanja ya Olonda. Tsegulani magaziniyo ndipo pitani pa “Zimene Zili M’magaziniyi” n’cholinga choti muphunzire nkhani zonse.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena