Malo Osungirako Zinthu Zakale Zokhudza Baibulo Kunthambi ya Belgium Akusonyeza Zimene Ena Anachita Kuti Ateteze Mawu A Mulungu
Onani mmene Yehova anadalitsira khama la omasulira Baibulo komanso amene analitulutsa amene analolera kuika moyo wawo pangozi kuti afalitse Baibulo.