Genesis 36:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Esau anakwatira ana aakazi a ku Kanani. Anakwatira Ada,+ mwana wamkazi wa Eloni, Muhiti.+ Anakwatiranso Oholibama,+ yemwe anali mwana wamkazi wa Ana komanso anali mdzukulu wa Zibeoni, Mhivi.
2 Esau anakwatira ana aakazi a ku Kanani. Anakwatira Ada,+ mwana wamkazi wa Eloni, Muhiti.+ Anakwatiranso Oholibama,+ yemwe anali mwana wamkazi wa Ana komanso anali mdzukulu wa Zibeoni, Mhivi.