Genesis 36:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mfumu Kora, Mfumu Gatamu ndi Mfumu Amaleki. Awa ndi amene anali mafumu akubanja la Elifazi+ mʼdziko la Edomu. Amenewa ndi ana a Ada.
16 Mfumu Kora, Mfumu Gatamu ndi Mfumu Amaleki. Awa ndi amene anali mafumu akubanja la Elifazi+ mʼdziko la Edomu. Amenewa ndi ana a Ada.