Genesis 36:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 mfumu Kora, mfumu Gatamu ndi mfumu Amaleki. Amenewa ndiwo anali mafumu a kubanja la Elifazi+ m’dziko la Edomu. Iwowa anali ana obadwa kwa Ada.
16 mfumu Kora, mfumu Gatamu ndi mfumu Amaleki. Amenewa ndiwo anali mafumu a kubanja la Elifazi+ m’dziko la Edomu. Iwowa anali ana obadwa kwa Ada.