Genesis 36:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Husamu atamwalira, Hadadi mwana wa Bedadi amene anagonjetsa Amidiyani+ mʼdera la Mowabu, anayamba kulamulira mʼmalo mwake, ndipo dzina la mzinda wake linali Aviti.
35 Husamu atamwalira, Hadadi mwana wa Bedadi amene anagonjetsa Amidiyani+ mʼdera la Mowabu, anayamba kulamulira mʼmalo mwake, ndipo dzina la mzinda wake linali Aviti.