Genesis 25:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tsopano Abulahamu anatenganso mkazi wina, dzina lake Ketura. 2 Patapita nthawi, mkaziyo anamuberekera Zimirani, Yokesani, Medani, Midiyani,+ Isibaki ndi Shuwa.+ Ekisodo 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako Farao anamva za nkhaniyi ndipo ankafuna kupha Mose. Koma Mose anathawa Farao nʼkupita kukakhala kudziko la Midiyani.+ Atafika kumeneko, anakhala pafupi ndi chitsime. Numeri 31:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uwabwezere+ Amidiyani chifukwa cha zimene anachitira Aisiraeli.+ Pambuyo pake udzaikidwa mʼmanda ngati mmene anachitira ndi makolo ako.”*+
25 Tsopano Abulahamu anatenganso mkazi wina, dzina lake Ketura. 2 Patapita nthawi, mkaziyo anamuberekera Zimirani, Yokesani, Medani, Midiyani,+ Isibaki ndi Shuwa.+
15 Kenako Farao anamva za nkhaniyi ndipo ankafuna kupha Mose. Koma Mose anathawa Farao nʼkupita kukakhala kudziko la Midiyani.+ Atafika kumeneko, anakhala pafupi ndi chitsime.
2 “Uwabwezere+ Amidiyani chifukwa cha zimene anachitira Aisiraeli.+ Pambuyo pake udzaikidwa mʼmanda ngati mmene anachitira ndi makolo ako.”*+