-
Genesis 36:39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Baala-hanani mwana wa Akibori atamwalira, Hadari anayamba kulamulira mʼmalo mwake, ndipo dzina la mzinda wake linali Pau. Mkazi wake dzina lake anali Mehetabele, mwana wa Matiredi. Matiredi anali mwana wamkazi wa Mezahabu.
-