Genesis 36:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Baala-hanani mwana wa Akibori atamwalira, Hadari anayamba kulamulira m’malo mwake, ndipo dzina la mzinda wake linali Pau. Mkazi wake dzina lake anali Mehetabele, mwana wa Matiredi. Matiredi anali mwana wamkazi wa Mezahabu.+
39 Baala-hanani mwana wa Akibori atamwalira, Hadari anayamba kulamulira m’malo mwake, ndipo dzina la mzinda wake linali Pau. Mkazi wake dzina lake anali Mehetabele, mwana wa Matiredi. Matiredi anali mwana wamkazi wa Mezahabu.+