Genesis 37:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno Isiraeli anati: “Pita ukaone ngati abale ako ali bwino. Ukaonenso ngati ziweto zili bwino ndipo udzandiuze.” Choncho anamuuza kuti anyamuke kuchigwa cha Heburoni+ ndipo ananyamuka nʼkulowera ku Sekemu. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:14 Nsanja ya Olonda,8/1/2014, tsa. 135/1/1987, tsa. 12 ‘Dziko Lokoma’, tsa. 7
14 Ndiyeno Isiraeli anati: “Pita ukaone ngati abale ako ali bwino. Ukaonenso ngati ziweto zili bwino ndipo udzandiuze.” Choncho anamuuza kuti anyamuke kuchigwa cha Heburoni+ ndipo ananyamuka nʼkulowera ku Sekemu.