Genesis 37:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiye Isiraeli anati: “Pita ukaone ngati abale ako ali bwino limodzi ndi nkhosa. Kenako ubwere udzandiuze.”+ Chotero, anamuuza kuti anyamuke kuchigwa cha Heburoni+ ndipo iye analowera ku Sekemu. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:14 Nsanja ya Olonda,8/1/2014, tsa. 135/1/1987, tsa. 12 ‘Dziko Lokoma’, tsa. 7
14 Ndiye Isiraeli anati: “Pita ukaone ngati abale ako ali bwino limodzi ndi nkhosa. Kenako ubwere udzandiuze.”+ Chotero, anamuuza kuti anyamuke kuchigwa cha Heburoni+ ndipo iye analowera ku Sekemu.