Genesis 41:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anaona ngʼombe 7 zikutuluka mumtsinje wa Nailo. Ngʼombezo zinali zooneka bwino komanso zonenepa, ndipo zinkadya udzu wamʼmbali mwa mtsinjewo.+
2 Iye anaona ngʼombe 7 zikutuluka mumtsinje wa Nailo. Ngʼombezo zinali zooneka bwino komanso zonenepa, ndipo zinkadya udzu wamʼmbali mwa mtsinjewo.+