Genesis 41:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pamenepo Yosefe anauza Farao kuti: “Maloto anu awiriwa tanthauzo lake ndi limodzi. Mulungu woona wakudziwitsani inu Farao zimene adzachite.+
25 Pamenepo Yosefe anauza Farao kuti: “Maloto anu awiriwa tanthauzo lake ndi limodzi. Mulungu woona wakudziwitsani inu Farao zimene adzachite.+