Genesis 41:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Chakudya chimenecho chidzakhala chakudya cha dzikoli pa zaka 7 zimene mʼdziko la Iguputo mudzakhale njala, kuti anthu ndi ziweto asadzafe ndi njalayo.”+
36 Chakudya chimenecho chidzakhala chakudya cha dzikoli pa zaka 7 zimene mʼdziko la Iguputo mudzakhale njala, kuti anthu ndi ziweto asadzafe ndi njalayo.”+