Genesis 41:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Farao anauzanso Yosefe kuti: “Farao ndine, koma popanda chilolezo chako, palibe wina aliyense amene angachite* chilichonse mʼdziko lonse la Iguputo.”+
44 Farao anauzanso Yosefe kuti: “Farao ndine, koma popanda chilolezo chako, palibe wina aliyense amene angachite* chilichonse mʼdziko lonse la Iguputo.”+