Genesis 41:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Kenako Farao anapatsa Yosefe dzina lakuti Zafenati-panea.* Anamʼpatsanso mkazi dzina lake Asenati+ yemwe anali mwana wa Potifera, wansembe wa mzinda wa Oni.* Ndipo Yosefe anayamba kuyangʼanira* dziko la Iguputo.+
45 Kenako Farao anapatsa Yosefe dzina lakuti Zafenati-panea.* Anamʼpatsanso mkazi dzina lake Asenati+ yemwe anali mwana wa Potifera, wansembe wa mzinda wa Oni.* Ndipo Yosefe anayamba kuyangʼanira* dziko la Iguputo.+