-
Genesis 42:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Iye anauza abale akewo kuti: “Taonani! Ndalama zanga andibwezera, izi zili mʼthumbazi!” Choncho mitima yawo inangoti myuu! ndipo anayamba kunjenjemera nʼkuyamba kufunsana kuti: “Kodi Mulungu akutichitira chiyani ife?”
-