Genesis 42:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ameneyo anauza abale ake kuti: “Taonani! Ndalama zanga andibwezera, izi zili m’thumbazi!” Pamenepo mitima yawo inangoti myuu! ndipo anayamba kunthunthumira+ n’kuyamba kufunsana kuti: “Kodi Mulungu akutichita chiyani ife?”+
28 Ameneyo anauza abale ake kuti: “Taonani! Ndalama zanga andibwezera, izi zili m’thumbazi!” Pamenepo mitima yawo inangoti myuu! ndipo anayamba kunthunthumira+ n’kuyamba kufunsana kuti: “Kodi Mulungu akutichita chiyani ife?”+