Levitiko 26:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 “‘Ndidzaika mantha m’mitima ya otsala pakati panu+ amene ali m’dziko la adani awo, moti adzathawa m’tswatswa wa tsamba louluka, ndipo adzathawa ngati kuti akuthawa lupanga. Pamenepo adzagwa popanda munthu wowathamangitsa.+ Luka 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndinachita zimenezi chifukwa ndinali kukuopani. Inutu ndinu munthu wouma mtima. Mumatenga zimene simunasungitse ndi kukolola zimene simunafese.’+
36 “‘Ndidzaika mantha m’mitima ya otsala pakati panu+ amene ali m’dziko la adani awo, moti adzathawa m’tswatswa wa tsamba louluka, ndipo adzathawa ngati kuti akuthawa lupanga. Pamenepo adzagwa popanda munthu wowathamangitsa.+
21 Ndinachita zimenezi chifukwa ndinali kukuopani. Inutu ndinu munthu wouma mtima. Mumatenga zimene simunasungitse ndi kukolola zimene simunafese.’+