Genesis 45:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chino ndi chaka chachiwiri cha njala padziko pano.+ Kutsogoloku kukubwera zaka zina 5 zimene anthu sadzalima kapena kukolola.
6 Chino ndi chaka chachiwiri cha njala padziko pano.+ Kutsogoloku kukubwera zaka zina 5 zimene anthu sadzalima kapena kukolola.