-
Genesis 45:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Choncho, mukauze bambo anga za ulemerero wanga wonse ku Iguputo kuno ndi zonse zimene mwaona. Ndiye fulumirani mukatenge bambo anga nʼkubwera nawo kuno.”
-