-
Genesis 45:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Choncho, mukauze bambo anga za ulemerero wanga wonse kuno ku Iguputo, ndi zonse zimene mwaona. Ndipo fulumirani mukatenge bambo anga n’kubwera nawo kuno.”
-