Genesis 45:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yosefe atatero, anakumbatira Benjamini mʼbale wake nʼkuyamba kulira. Nayenso Benjamini analira atakumbatira mʼbale wakeyo.+
14 Yosefe atatero, anakumbatira Benjamini mʼbale wake nʼkuyamba kulira. Nayenso Benjamini analira atakumbatira mʼbale wakeyo.+