Genesis 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Madzi anapitirizabe kuchepa mpaka mwezi wa 10. Mʼmwezi wa 10 umenewo, pa tsiku loyamba la mweziwo, nsonga za mapiri zinaonekera.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:5 Nsanja ya Olonda,8/1/2013, tsa. 145/15/2003, tsa. 5
5 Madzi anapitirizabe kuchepa mpaka mwezi wa 10. Mʼmwezi wa 10 umenewo, pa tsiku loyamba la mweziwo, nsonga za mapiri zinaonekera.+