Genesis 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Utuluke limodzi ndi zamoyo zamtundu uliwonse+ zimene uli nazo. Utuluke limodzi ndi zamoyo zouluka, zinyama ndi zonse zokwawa padziko lapansi, kuti zichulukane padziko lapansi, ziberekane ndipo zikhale zambiri padziko lapansi.”+
17 Utuluke limodzi ndi zamoyo zamtundu uliwonse+ zimene uli nazo. Utuluke limodzi ndi zamoyo zouluka, zinyama ndi zonse zokwawa padziko lapansi, kuti zichulukane padziko lapansi, ziberekane ndipo zikhale zambiri padziko lapansi.”+