-
Genesis 22:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ndiyeno Isaki analankhula ndi Abulahamu bambo ake kuti: “Bambo!” Abulahamu anayankha kuti: “Lankhula mwana wanga.” Choncho iye anafunsa kuti: “Moto ndi nkhuni nʼzimenezi, nanga nkhosa yokapereka nsembe yopsereza ili kuti?”
-