Genesis 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Isaki analankhula ndi Abulahamu bambo ake kuti: “Bambo!”+ Abulahamu anayankha kuti: “Lankhula mwana wanga.”+ Chotero iye anafunsa kuti: “Moto ndi nkhuni n’zimenezi, nanga nkhosa yokapereka nsembe yopsereza ili kuti?”+
7 Ndiyeno Isaki analankhula ndi Abulahamu bambo ake kuti: “Bambo!”+ Abulahamu anayankha kuti: “Lankhula mwana wanga.”+ Chotero iye anafunsa kuti: “Moto ndi nkhuni n’zimenezi, nanga nkhosa yokapereka nsembe yopsereza ili kuti?”+