Ekisodo 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nkhosa yanuyo ikhale yopanda chilema,+ yamphongo, yachaka chimodzi.+ Mungatenge mwana wa nkhosa kapena wa mbuzi. Aroma 8:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Monga mmene Malemba amanenera kuti: “Chifukwa cha inu, tikuphedwa nthawi zonse. Takhala ngati nkhosa zokaphedwa.”+
5 Nkhosa yanuyo ikhale yopanda chilema,+ yamphongo, yachaka chimodzi.+ Mungatenge mwana wa nkhosa kapena wa mbuzi.
36 Monga mmene Malemba amanenera kuti: “Chifukwa cha inu, tikuphedwa nthawi zonse. Takhala ngati nkhosa zokaphedwa.”+