-
Genesis 24:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 nʼkunena kuti: “Atamandike Yehova, Mulungu wa mbuye wanga Abulahamu, chifukwa sanasiye kusonyeza mbuye wanga chikondi chokhulupirika komanso nthawi zonse amakwaniritsa zimene wamulonjeza. Yehova wanditsogolera kunyumba kwa abale a mbuye wanga.”
-