Genesis 24:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 n’kunena kuti: “Atamandike Yehova,+ Mulungu wa mbuyanga Abulahamu, amene sanasiye kusonyeza mbuyanga kukoma mtima kosatha ndi kukhala wokhulupirika kwa iye. Pa ulendo wangawu, Yehova wanditsogolera kunyumba kwa abale a mbuyanga.”+
27 n’kunena kuti: “Atamandike Yehova,+ Mulungu wa mbuyanga Abulahamu, amene sanasiye kusonyeza mbuyanga kukoma mtima kosatha ndi kukhala wokhulupirika kwa iye. Pa ulendo wangawu, Yehova wanditsogolera kunyumba kwa abale a mbuyanga.”+