Genesis 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Anawonjezera kuti:“Adalitsike Yehova,+ Mulungu wa Semu,Ndipo Kanani akhale kapolo kwa iye.+ Salimo 72:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Adalitsike Yehova Mulungu, Mulungu wa Isiraeli,+Iye yekha amene akuchita ntchito zodabwitsa.+ Luka 1:68 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 “Atamandike Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ chifukwa wacheukira anthu ake+ ndi kuwapatsa chipulumutso.+
68 “Atamandike Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ chifukwa wacheukira anthu ake+ ndi kuwapatsa chipulumutso.+