Genesis 30:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mwanayo atabadwa, Leya anati: “Mulungu wandipatsa mphoto* chifukwa ndapereka kapolo wanga kwa mwamuna wanga.” Choncho Leya anapatsa mwanayo dzina lakuti Isakara.*+
18 Mwanayo atabadwa, Leya anati: “Mulungu wandipatsa mphoto* chifukwa ndapereka kapolo wanga kwa mwamuna wanga.” Choncho Leya anapatsa mwanayo dzina lakuti Isakara.*+