Genesis 33:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako Yakobo ananyamuka ulendo wopita ku Sukoti.+ Kumeneko anamanga nyumba yake ndi makola a ziweto zake. Nʼchifukwa chake malowo anawapatsa dzina lakuti Sukoti.*
17 Kenako Yakobo ananyamuka ulendo wopita ku Sukoti.+ Kumeneko anamanga nyumba yake ndi makola a ziweto zake. Nʼchifukwa chake malowo anawapatsa dzina lakuti Sukoti.*