Genesis 33:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsopano Yakobo ananyamuka ulendo wopita ku Sukoti.+ Kumeneko anamanga nyumba yake ndi makola a ziweto zake.+ N’chifukwa chake malowo anawatcha kuti Sukoti.*
17 Tsopano Yakobo ananyamuka ulendo wopita ku Sukoti.+ Kumeneko anamanga nyumba yake ndi makola a ziweto zake.+ N’chifukwa chake malowo anawatcha kuti Sukoti.*