Genesis 33:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamalopo anamangapo guwa lansembe nʼkulitchula kuti Mulungu, Mulungu wa Isiraeli.+