Genesis 33:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Atatero, anamangapo guwa lansembe n’kulitcha Mulungu, Mulungu wa Isiraeli.+