Ekisodo 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iyeyo ndi amene azikalankhula kwa anthu mʼmalo mwa iwe. Choncho adzakhala wokulankhulira, ndipo iwe udzakhala ngati Mulungu kwa iye.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:16 Nsanja ya Olonda,3/15/2004, tsa. 24
16 Iyeyo ndi amene azikalankhula kwa anthu mʼmalo mwa iwe. Choncho adzakhala wokulankhulira, ndipo iwe udzakhala ngati Mulungu kwa iye.+