Ekisodo 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iyeyo ndiye azikalankhula kwa anthu m’malo mwa iwe.+ Choncho adzakhala ngati kamwa lako, ndipo iwe udzakhala ngati Mulungu kwa iye.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:16 Nsanja ya Olonda,3/15/2004, tsa. 24
16 Iyeyo ndiye azikalankhula kwa anthu m’malo mwa iwe.+ Choncho adzakhala ngati kamwa lako, ndipo iwe udzakhala ngati Mulungu kwa iye.+