-
Ekisodo 10:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Atatero Yehova anachititsa kuti mphepo yamphamvuyo iziwomba kuchokera kumadzulo ndipo inatenga dzombelo nʼkukaliponya mʼNyanja Yofiira. Mʼdera lonse la Iguputo simunatsale dzombe ngakhale limodzi.
-