Ekisodo 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho Mose ndi Aroni anauza Aisiraeli onse kuti: “Madzulo ano mudziwa kuti Yehova ndi amene anakutulutsani mʼdziko la Iguputo.+
6 Choncho Mose ndi Aroni anauza Aisiraeli onse kuti: “Madzulo ano mudziwa kuti Yehova ndi amene anakutulutsani mʼdziko la Iguputo.+