Ekisodo 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho Mose ndi Aroni anauza ana onse a Isiraeli kuti: “Madzulo ano mudziwa kuti Yehova ndiye anakutulutsani m’dziko la Iguputo.+
6 Choncho Mose ndi Aroni anauza ana onse a Isiraeli kuti: “Madzulo ano mudziwa kuti Yehova ndiye anakutulutsani m’dziko la Iguputo.+