Ekisodo 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotero ndidzakutengani kukhala anthu anga,+ ndi kukusonyezani kuti ndine Mulungu.+ Inuyo mudzadziwadi kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndidzakutulutsani mu Iguputo, ndi kukuchotserani goli lawo.+ Numeri 16:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno Mose anati: “Mudziwira izi kuti Yehova ndiye anandituma kuti ndichite zonsezi,+ ndiponso kuti si za mumtima mwanga ayi:+ Salimo 77:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mwatsogolera anthu anu ngati nkhosa,+Kudzera mwa Mose ndi Aroni.+ Yesaya 63:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo anayamba kukumbukira masiku akale, masiku a Mose mtumiki wake, ndipo anafunsa kuti: “Kodi amene anawatulutsa m’nyanja+ pamodzi ndi abusa a anthu ake uja, ali kuti?+ Ali kuti amene anaika mzimu wake woyera mwa iye?+
7 Chotero ndidzakutengani kukhala anthu anga,+ ndi kukusonyezani kuti ndine Mulungu.+ Inuyo mudzadziwadi kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndidzakutulutsani mu Iguputo, ndi kukuchotserani goli lawo.+
28 Ndiyeno Mose anati: “Mudziwira izi kuti Yehova ndiye anandituma kuti ndichite zonsezi,+ ndiponso kuti si za mumtima mwanga ayi:+
11 Iwo anayamba kukumbukira masiku akale, masiku a Mose mtumiki wake, ndipo anafunsa kuti: “Kodi amene anawatulutsa m’nyanja+ pamodzi ndi abusa a anthu ake uja, ali kuti?+ Ali kuti amene anaika mzimu wake woyera mwa iye?+